Quest (MW)
Suntha
[Intro]
Ah, ah
Mm yeah

[Chorus]
Suntha phazi ndipondepo
Ndikumbatile kuli mphepo
Osawona nyengo, zawina usaganizekonso
Suntha phazi ndipondepo
Ndikumbatile kuli mphepo
Osawona nyengo, zawina usaganizekonso

[Verse 1]
Nkazi uli fine iwe ungokhala wa ine
Tachoka kutali uthokhala mboni ya ine
This time I'm taking this for serious
So slowly girl I'm not so furious
Ndinkapanga zachibwana pano ndili Serious
Ntangokumana ndi iwe
Moyo wanga wachimfana koma pano ndanakula chifukwa cha zomwe umandiwuza iwe
Mmene umandiyikila pa easy
Zimandiwaza ukamandi teaser, ndisaname nkazi umandiliza
Misozi yachimwemwe yangodzadza muntima
Ndakumana naye nkazi yemwe ndimafuna

[Chorus]
Suntha phazi ndipondepo
Ndikumbatile kuli mphepo
Osawona nyengo, zawina usaganizekonso
Suntha phazi ndipondepo
Ndikumbatile kuli mphepo
Osawona nyengo, zawina usaganizekonso

[Bridge]
Yеah eh, yeah eh, yah
Inе ndili ready, yeah

[Verse 2]
Mufuse Brown ine ndimakonda heavy
Mfuse Ten May akuwuza usandileke
Babe you're my desire
Nzakuyimbila ngati kwaya
Pali iwe payaka fire
Ndipo sinfuna kuvaya
Everytime you pull up make me forget about my ex
Everytime you pull up make me know that I'm the best
Nde m'mene undiyikila pa easy
Umandipangitsa kukhala shasha
Kuwoneka ngati wamakwacha
Umandipatsa mphavu ngati msilikali
Mawonekedwe ako iwe ndipatali
[Chorus]
Suntha phazi ndipondepo
Ndikumbatile kuli mphepo
Osawona nyengo, zawina usaganizekonso
Suntha phazi ndipondepo
Ndikumbatile kuli mphepo
Osawona nyengo, zawina usaganizekonso

[Outro]
(Loyal.. loyal hustle the factory)