[Intro]
Mm-mm-mm
Yah, yeah, eh, eh, eh
Yeah, eh, eh
Mm-mm-mm
(Loyal--- loyal hustle the factory)
Eh-yah, Quest
[Pre-Chorus]
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko (Mm, hmm)
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko
[Chorus]
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step
[Verse 1]
Ndilibe jealous, jealous, eh
Ndifuna ndikawoneko ku nsanje
Zifukwa zoferazi, 'ferazi, eh
Ndikawoneko phiri la Mulanje, yeah
Tikadyеko ma papaya, yeah
Thyolo, Zomba mpaka Blantyre, yeah
Chikwawa ndе tansiya, yeah
Tikafika Dedza tikathyole dance ah-huh (Eh)
Kungofika ndiku Lilongwe (Ah-huh)
Malawi ndikuwala mbe (Ah-huh)
Salima mpakana ku Nkhatabay
Tikafika ku Likoma kumakhala phe
Ku Nkhotakota, eh, tikayipota, eh
Nde kuchitipa Kapesa tikasipa, eh
[Pre-Chorus]
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko (Mm, hmm)
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko
[Chorus]
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step
[Verse 2]
Mzuzu, Mzimba
Wanakazi wanikhumba
Sound yane wayikhumba
Wayiphulikira umu gumbagumba
My phone is ringing
Kuli nkaka ndi uchi ku Nchinji
Kasungu I be trappin', I be moving around I ain't stoppin'
Tikafike nde ku Dowa
Kumadisi ku Mangochi ndakusowa
Balaka ndikulowa potuluka chaku Mwanza ndikudzera
Warm heart of Africa, ask around it is Malawi
Chiradzulu tikafika, atate tipatseni nthawi
Malawi I love you, you're the reason I [?] put a tattoo, yeah
Uku ndi kwathu, kukunyadira that is what what I do, yeah
[Pre-Chorus]
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko (Mm, hmm)
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko
[Chorus]
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step (Ponya)
Tiye ponya step
[Outro]
(Loyal--- loyal hustle the factory)