Quest (MW)
Sendera
[Verse 1]
Yah
Muntima mwanga zimafuso zili mbwe
Ndizikhala bwanji ndekha?
Kuyambira tsiku lomwe unandileka
M'moyo mwanga suzutheka
Nzovuta kuyiwala tima memories
Utabwelera m'moyomu nde ndingafile victory
Ndizolowere munthu wina
Ine singakwanise kapena nfuse iwe mwina, yah
Ndizicheza ndi wina
Ine singakwanise kuti ndikawoneso wina

[Chorus]
Ndikupempha sendera
Ntima mwanga unakweza mbendera
Zimandiwaza ukandisekelera
Ndipomwe mtima wanga unathera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera

[Verse 2]
Sendera pafupi
Thupi langa limandiwuza lasowa lako thupi
Achibale amandifusa, ukuyenda bwanji wekha
Mesa munkayenda two people?
Ndinali munthu ine nde chifukwa cha iwe
Mavuto nde ndinkayiwala chifukwa cha iwe
Ndasowa kukhala nawe limozitu everyday
Chikondi chako chinali chopanda holiday
Ngati zili zotheka babe
I'm sorry, I'm sorry, I'm sorry, I'm sorry
Sindizabwereza zinkhani
Ma story, ma story, ma story, ma story
Babe give me one chance, eh
All I need is a one dance, eh
Ndikufuna m'moyo mwanga, eh
Ndiyambileso ndiyambireso kunjanja, eh
[Chorus]
Ndikupempha sendera
Mumtima mwanga unakweza mbendera
Zimandiwaza ukandisekelera
Ndipomwe mtima wanga unathera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera

[Outro]
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
Sendera pafupi 'fupi 'fupi
Sendera
(Loyal.. loyal hustle the factory)