[Intro: Quest]
(Loyal.. loyal hustle the factory)
Mundilore ndimtenge
Mundilore ndimtenge
[Chorus: Quest]
Mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Oh mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Oh Mama
Mundilore Ndimtenge, mundilore ndimtenge
Mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Oh mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Oh mama
Mundilore ndimtenge, ndimtenge
Oh mama
Mundilore ndimtenge, ndimtenge
[Verse 1: Quest]
Mama mundilore ndimtenge
Nkamuveke mphete
Ndivaye naye pa den, ayy
She be coming in my dreams everytime I sleep like everyday
Mumy ndili ndinthanana mwana wanu sindingamusiye
Believe me
Pankhani ya chikondi I got a degree
As you can see
Kamwana kanu ndeno ndika VIP
Kaya mundiwuza mfuna ng'ombe
Ndatopa nazo izi zomuzembera
Runnin' of air, she my inhaler
She always got my back, kutchera [?]
[Bridge: Quest]
Mama can you please give me your mwana
She running round my head like bandana
Ndikulonjeza nsiya zibwana
Mama I need your answer
Tell me right now
[Chorus: Quest]
Mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Oh mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Oh Mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Oh mama
Mundilore ndimtenge, mundilore ndimtenge
Oh mama
Mundilore ndimtenge, ndimtenge
Oh mama
Mundilore ndimtenge, ndimtenge
[Verse 2: Hyphen]
Mama
Mundilore ndimtenge
Zolemetsa mtima wake ndi nseze
Singalore agone njala ine ndi mlenje
All I need is your blessing
I already got her attention
Look look
Ndikudziwa mbiri yanga siyosililika
Ndikudziwa nkhani nkuchilimika
Ndikudziwa mukukayika zondipatsa mita
Muzawona powomola, musayang'ane mphika
Kachi Firika
I know she is special
Kufusa [?]
I never thought that it would get to this level
Pomwe mumafunapo ndimfikitsepo
Kwakuru mwachita let me take over
Munalera mowopa Yehova
Zimakhalidwe za Mkomnya when she stays over
Za u player ndinazipachika, gamer over