Quest (MW)
Tsutsa
[Chorus: Quest]
Kodi mesa munkatsutsa?
Zoti ndi dolo
Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story?
Kodi mesa munkatsutsa?
Limakwana la fourty
Osaphweketsa yanzako iliyose story
Kodi mesa munkatsutsa?
Zoti ndi dolo
Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story?
Kodi mesa munkatsutsa?
Limakwana la fourty
Osaphweketsa yanzako iliyose story

[Verse 1: Quest]
Ankandiseka nkavala zigamba
Trouser lopanda lamba
Nkhani zanga nkamakamba
Ankaona lachokera banja langa
Nkawawuza amasintha ndi masiku
Chonde mundivele musawone msinkhu
Koma ayi ankandiseka
Ndipo ankati nzosatheka
Koma Mulungu si nzako
Program yake nde siyako
Amadalitsa osasiyako
Samapanga nawo zazisankho

[Chorus: Quest]
Kodi mesa munkatsutsa?
Zoti ndi dolo
Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story?
Kodi mesa munkatsutsa?
Limakwana la fourty
Osaphweketsa yanzako iliyose story
Kodi mesa munkatsutsa?
Zoti ndi dolo
Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story?
Kodi mesa munkatsutsa?
Limakwana la fourty
Osaphweketsa yanzako iliyose story
[Verse 2: Valine]
Munandisiya ndekha
Pomwe ndinkakufunani osapezeka
Maganizo kupenga
Mayeselo ake nde sindinkavetsa
Kugona ndi njala
Kusowa kokhala
Ku kamba za nzeru ankayesa ndi misala
Yah, yah, yah, yah, yah, yah
Things change somehow
Mulungu si munthu
Sayiwala munthu
Everywhere you're lonely
Ndiyekha angakukonde

[Chorus: Quest]
Kodi mesa munkatsutsa?
Zoti ndi dolo
Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story?
Kodi mesa munkatsutsa?
Limakwana la fourty
Osaphweketsa yanzako iliyose story
Kodi mesa munkatsutsa?
Zoti ndi dolo
Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story?
Kodi mesa munkatsutsa?
Limakwana la fourty
Osaphweketsa yanzako iliyose story