[Pre-Chorus: Quest]
Ah, ah, ah
Akumatisowa muma show
Tikafika amafila bho
Akumayimba ma phone
Kwawo tifikako litilo?
Akumatisowa muma show (Muma show, muma show)
Tikafika amafila bho (Amafila bho)
Akumayimba ma phone (Ma phone, ma phone)
Kwawo tifikako litilo? (Tifika litilo?)
[Quest: Chorus]
Tikafika timayatsa moto, moto, moto (Fire)
Moto, moto, moto (Fire, fire, fire)
Moto, moto, moto (Fire)
Moto, moto, moto (Fire, fire, fire)
[Verse 2: K Banton]
Timayipatsa moto unandi
Timayakitsa fire illuminati
Mubwere ku show mutipeza tili mkati
Akazi oyambilira azalowa ndi angati?
Ma guy akufusa ndiwe friend ndi Quest?
Nakutumizilapotu friend request
Nanga bwanji ukucheza m'ma fans, ndiwe friendly guest?
Wandipeza pa stage ndi Gin koma ndine friend ndi Best
Kudzuka kusuzumila calendar
Kodi organizer ata-halle nda?
Akakhala ajawa a surrender
Ma guy tikafika amapenga
Amatisowa tikakhala tili pa easy
Amatifila tikakhala tili m'ma busy
[Pre-Chorus: Quest]
Akumatisowa muma show
Tikafika amafila bho
Akumayimba ma phone
Kwawo tifikako litilo?
Akumatisowa muma show (Muma show, muma show)
Tikafika amafila bho (Amafila bho)
Akumayimba ma phone (Ma phone, ma phone)
Kwawo tifikako litilo? (Tifika litilo?)
[Chorus: Quest]
Tikafika timayatsa moto, moto, moto (Fire)
Moto, moto, moto (Fire, fire, fire)
Moto, moto, moto (Fire)
Moto, moto, moto (Fire, fire, fire)
[Verse 3: Dette Flo]
Socks yanga kuikweza ndege daily
I been on ma highest shit lately
Sweeter the juice blacker the berry
Got the whole thang ndiwanyemele
Highest in the room pano sakutipeza tasintha level
They like the move unpredictable they can never tell it
We been shootin' been shootin' really miss ya
Tokha tasiyanisa munafika
Ma big stepper ma thipa mulipati
Errthang we been on kumveka mwachi planie
They like how you doin' up there?
Zomwe mumapanga sizophweka
Shlime bidness that way, muli mkati software
I wanna see it pilin' then I see you smilin'
You gon' dive in, we goin' crazy, goin' retarded
[Pre-Chorus]
Akumatisowa muma show
Tikafika amafila bho
Akumayimba ma phone
Kwawo tifikako litilo?
Akumatisowa muma show (Muma show, muma show)
Tikafika amafila bho (Amafila bho)
Akumayimba ma phone (Ma phone, ma phone)
Kwawo tifikako litilo? (Tifika litilo?)
[Chorus: Quest]
Tikafika timayatsa moto, moto, moto (Fire)
Moto, moto, moto (Fire, fire, fire)
Moto, moto, moto (Fire)
Moto, moto, moto (Fire, fire, fire)