[Intro: Namadingo]
Alipo, alipo ondi-
Alipo, alipo ondi-
[Verse 1: Namadingo]
Alipo ondidelera
M’maso mwawo ndimachepera
Akuti nyimbo zanga samvera
Ndi-ndi, ndipo sine oyenera kumanditchula dokotala
Ndilibe PhD papepala
Angondipatsa udokotalawu
Nde wina akamva Doc sasangalala
Eti mpaka kunditchula kuti wamsala
Ndingothokoza Mulungu oyera amandikondera
Madalitso akubwera tikulemera
Namadingo most followed mumfuse [?]
[Chorus: Namadingo]
Adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)

[Verse 2: Ty Grin & Namadingo]
Rrr-rah, dats de fire dere
Mfumu yazinyawu ija
Flow so sick I need a doctor to feature
I am not an average joe, they pay me what you make in a year for a show
In a deck of cards I’m the jokеr
I’m the extremе opposite of mediocre
Simungamake ndine messi pa soccer
Grin ndi messi pa soccer (Yeah)
Too many international awards
I’m representing Malawi, your bro
Doing this till I grow old
Nanga timea squire? Ndili pa billboard
[Chorus: Namadingo]
Ena adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)
Ena adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)
[Verse 2: Ty Grin & Namadingo]
Muliponso ena all over the world
Mumadeleledwa kuchepetsedwa
If you visualize it, you’re bound to do it
Life’s a jungle, me I rumble through it
If I can do it, y’all can do it
From the frontline, put your back into it
[Chorus: Namadingo]
Ena adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)
Ena adzavomeleza too late (Pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (Pano iwo ndi lalala)
[Outro: Ty Grin]
Joe Gwaladi aseh uli bho?