The Very Best
Yalira
Mwalandilidwa nonse, dsina langa ndine
Esau Mwamwaya ndi Radioclit, The Very Best
Tiyeni tonse tivine danse poti moto wayaka!

Belita, Angela ndi Rita tabwera
Joe, Jack ndi Mick tabwera
Awiri! Awiri! Tivine limodzi
Ponda! Ponda! Yalira ng'oma

Kodi wawa, magaye, mwatani kodi mwakhala
Khumakhuma
Mwangotsamira mtengo
M'maso muli penyapenya

London iwe
New York iwe
Paris iwe
Lilongwe iwe

Ndati tikumbukenso mwa anzathu ena omwe
Anatisiya kale, abale oimbawa anatisiya chabe
M'mathupi, koma nyimbo zawo zizakhala zikumueka
Mpakana kalekale

Fumulani iwe
Gwilani iwe
Bob Marley iwe
Matafale iwe