Ndikudziwa timacheza
Ndikudziwa unandiuza
Mtima wako unasweka
Pano chikondi suchifuna
Koma nanga ndipange bwanji
Tandiuze ndipange bwanji
Nthawi yonseyi
Ndinkayesa ukhala chabe friend
Ndadziwa pano ndinapanga mistake
Ndili ndi mantha kodi sukhumudwa iwe
Ndikakuuza ndimakufuna
Ndikakuuza ndimakufuna
Koma nanga ine ndipange bwanji
Tandiuze ine ndipange bwanji
Ooh I fell in love ndipo si za jokes
Mami ine ndipange bwanji
Kuseli, kuseli
Ndimaka dumpha dumpha ndikakuona
Chikondwelelo chake cha mpeni (uh)
Mami ukandigunda thupi langa limagwidwa nyesi (uh)
Ndipo ukandi caller phone singalile kawili yeah
Nthawi yonseyi
Ndinkayesa ukhala chabe friend
Ndadziwa pano ndinapanga mistake
Ndili ndi mantha kodi sukhumudwa iwe
Ndikakuuza ndimakufuna
Ndikakuuza ndimakufuna
Koma nanga ine ndipange bwanji
Tandiuze ine ndipange bwanji
Ooh I fell in love ndipo si za jokes
Mami ine ndipange bwanji
Please don't call me your brother ndikawulula
Zonse za ku mtima kwanga ndikakhuthula
Chonde usandikwiyile nkundituluka
Ndayesesa kupilila osakuuza
Chabe mami ndimakukonda
Baby ine ndimakukonda
Ndimakukonda konda