[Intro]
Classic!
Mmm-mm… Orama!
Yobezani
Eeeh!
Emmanuel, yeah!
[Verse 1: Orama]
Eeeh! akandiwona
N’takhumudwa n’sakukondwa
Kumakondwera iwowa
Kumandijeda iwowa
Eeeh! Mbuye wanga ndi Mtondo, ndi Mtondo, ndi Mtondo
Tate wanga ndi Leader, ndi leader, ndi Leader
Tate wanga ndi Leader
Ndipo sindidzalira
Ndithu sadzandisiya
Ine ndikuyamika!
[Chorus: Orama]
Yeah, I gotta be honest
Siwina koma Inuyo
Sin’zitengera chizolowezi
I owe it all to You, Lord!
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
[Verse 2: Yobezani]
Ndilibe chifukwa chodzitamira
‘Cause I know I’m just a product of Your Grace
Chipanda Inu bwezi nditataika
No doubt, yeah I coulda been some waste
N’nalawa ubwino Wanu
Munandigula ndi mwazi n’kundipanga Wanu
Munandipatsa moyo wina, now I’m brand new
And I’m enjoying its fullness, sorry Dan Lu
Yeah! I acknowledge it’s all You, Lord
M’mene n’nali mu dead-end munali clue, Lord
Ndikupanga sеlf-searching munali Google
Till I found myself еngulfed in Your cool Love
Ngiyabonga!
[Chorus: Orama]
Yeah, I gotta be honest
Siwina koma Inuyo
Sin’zitengera chizolowezi
I owe it all to You, Lord!
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
[Verse 3: Emmanuel]
Kundiombola m’zikhomo
Adani anatseka, mwanditsegulira khomo
Nkhawa n’napachika ndimayenda mu zisomo
Ndi Yesu zonse zinayera n’mwazi osati Omo
Zomwe mwachita pa moyo wanga indedi n’zambirimbiri
Mwakuza malire anga, ndikundisinthanso mbiri
Adani kundipinga n’cholinga choti andikole mu goli
Koma munandi-saver m’manja mwawo, munawayika zigoli (haha!)
Ndadza pano kunena zikomo
Mdalitso Wanu umabweretsa bata m’timamo
Sindikulabada olo dyabu akoke tsinya
Chomwe ndikuchita nkhumupokela Chiuta wa ku chanya
[Chorus: Orama]
Yeah, I gotta be honest
Siwina koma Inuyo
Sin’zitengera chizolowezi
I owe it all to You, Lord!
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika
Yamika, ndikuyamika